-
1 Mafumu 5:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Tsopano lamulani kuti anthu andidulire mitengo ya mkungudza ya ku Lebanoni.+ Antchito anga adzakhala limodzi ndi antchito anu ndipo ndidzakupatsani malipiro a antchito anu malingana ndi zonse zomwe munganene. Inuyo mukudziwa bwino kuti pakati pathu palibenso anthu odziwa kudula mitengo ngati Asidoni.”+
-