Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Anapitiriza kumanga nyumbayo kuti aimalize,+ ndipo mkati mwa nyumbayo anamangamo ndi matabwa ndi mitanda ya mitengo ya mkungudza.+

  • 1 Mafumu 6:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Chipinda chamkati chinali mikono 20 m’litali, mikono 20 m’lifupi+ ndi mikono 20 kutalika kwake. Chipindacho anachikuta ndi golide woyenga bwino,+ komanso anakuta guwa lansembe+ ndi matabwa a mkungudza.

  • 2 Mbiri 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Munditumizirenso matabwa a mitengo ya mkungudza,+ mitengo ina yofanana ndi mkungudza,+ ndiponso a mitengo ya m’bawa+ kuchokera ku Lebanoni,+ popeza ndikudziwa bwino kuti antchito anu ndi akatswiri odziwa kudula mitengo ya ku Lebanoni,+ (antchito anga adzagwira ntchito pamodzi ndi antchito anu,)

  • Salimo 104:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mitengo ya Yehova imathiriridwa bwino,

      Mikungudza ya ku Lebanoni imene iye anabzala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena