Salimo 92:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wolungama adzakula ngati mtengo wa kanjedza,+Ndipo adzakula kwambiri ngati mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni.+ Ezekieli 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzaibzala pamwamba pa phiri lalitali la ku Isiraeli+ ndipo idzachita nthambi ndi kubereka zipatso+ n’kukhala mtengo waukulu wa mkungudza.+ Mbalame zamitundu yonse zizidzakhala pansi pa mtengowo ndi mumthunzi wa masamba ake.+
12 Wolungama adzakula ngati mtengo wa kanjedza,+Ndipo adzakula kwambiri ngati mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni.+
23 Ndidzaibzala pamwamba pa phiri lalitali la ku Isiraeli+ ndipo idzachita nthambi ndi kubereka zipatso+ n’kukhala mtengo waukulu wa mkungudza.+ Mbalame zamitundu yonse zizidzakhala pansi pa mtengowo ndi mumthunzi wa masamba ake.+