Salimo 52:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ine ndidzakhala ngati mtengo waukulu wa maolivi+ wa masamba obiriwira m’nyumba ya Mulungu.Ndidzakhulupirira kukoma mtima kosatha kwa Mulungu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Yesaya 65:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Sadzamanga wina n’kukhalamo. Sadzabzala wina n’kudya. Pakuti masiku a anthu anga adzakhala ngati masiku a mtengo,+ ndipo anthu anga osankhidwa mwapadera adzapindula mokwanira ndi ntchito ya manja awo.+ Hoseya 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nthambi zake zidzaphukira ndipo adzakhala ndi ulemerero ngati mtengo wa maolivi.+ Fungo lake lonunkhira lidzakhala ngati mtengo wa ku Lebanoni.
8 Koma ine ndidzakhala ngati mtengo waukulu wa maolivi+ wa masamba obiriwira m’nyumba ya Mulungu.Ndidzakhulupirira kukoma mtima kosatha kwa Mulungu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
22 Sadzamanga wina n’kukhalamo. Sadzabzala wina n’kudya. Pakuti masiku a anthu anga adzakhala ngati masiku a mtengo,+ ndipo anthu anga osankhidwa mwapadera adzapindula mokwanira ndi ntchito ya manja awo.+
6 Nthambi zake zidzaphukira ndipo adzakhala ndi ulemerero ngati mtengo wa maolivi.+ Fungo lake lonunkhira lidzakhala ngati mtengo wa ku Lebanoni.