Salimo 92:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wolungama adzakula ngati mtengo wa kanjedza,+Ndipo adzakula kwambiri ngati mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni.+ Salimo 92:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zinthu zidzapitiriza kuwayendera bwino ngakhale atachita imvi,+Adzakhalabe onenepa ndi athanzi,+ Chivumbulutso 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye adzapukuta misozi+ yonse m’maso mwawo, ndipo imfa sidzakhalaponso.+ Sipadzakhalanso kulira,+ kapena kubuula, ngakhale kupweteka. Zakalezo zapita.”+
12 Wolungama adzakula ngati mtengo wa kanjedza,+Ndipo adzakula kwambiri ngati mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni.+
14 Zinthu zidzapitiriza kuwayendera bwino ngakhale atachita imvi,+Adzakhalabe onenepa ndi athanzi,+ Chivumbulutso 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye adzapukuta misozi+ yonse m’maso mwawo, ndipo imfa sidzakhalaponso.+ Sipadzakhalanso kulira,+ kapena kubuula, ngakhale kupweteka. Zakalezo zapita.”+
4 Iye adzapukuta misozi+ yonse m’maso mwawo, ndipo imfa sidzakhalaponso.+ Sipadzakhalanso kulira,+ kapena kubuula, ngakhale kupweteka. Zakalezo zapita.”+