Salimo 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndakhulupirira kukoma mtima kwanu kosatha.+Mtima wanga ukondwere chifukwa cha chipulumutso chanu.+ Salimo 147:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova amasangalala ndi anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera kukoma mtima kwake kosatha.+
5 Koma ine ndakhulupirira kukoma mtima kwanu kosatha.+Mtima wanga ukondwere chifukwa cha chipulumutso chanu.+