1 Mafumu 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso, anagawa chigawo cha mikono 20 kumbuyo kwa nyumbayo ndi matabwa a mkungudza, kuchokera pansi mpaka kudenga. Nyumbayo anaimangira chipinda chamkati,+ chotchedwa Malo Oyera Koposa.+
16 Komanso, anagawa chigawo cha mikono 20 kumbuyo kwa nyumbayo ndi matabwa a mkungudza, kuchokera pansi mpaka kudenga. Nyumbayo anaimangira chipinda chamkati,+ chotchedwa Malo Oyera Koposa.+