1 Mafumu 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso, anamanga zipinda kuzungulira khoma lonse la nyumbayo, kuzungulira makoma onse akunja a chipinda chachikulu ndi chipinda chamkati.+ Anamanga zipinda zam’mbali+ zosanjikizana kuzungulira nyumba yonseyo. 2 Mbiri 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ M’litali mwake chinali mikono 20+ mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Choncho m’lifupi mwake, chipindacho chinali mikono 20, ndipo anachikuta ndi golide wabwino wokwanira matalente* 600.
5 Komanso, anamanga zipinda kuzungulira khoma lonse la nyumbayo, kuzungulira makoma onse akunja a chipinda chachikulu ndi chipinda chamkati.+ Anamanga zipinda zam’mbali+ zosanjikizana kuzungulira nyumba yonseyo.
8 Kenako anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ M’litali mwake chinali mikono 20+ mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Choncho m’lifupi mwake, chipindacho chinali mikono 20, ndipo anachikuta ndi golide wabwino wokwanira matalente* 600.