2 Mbiri 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako iye anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ Mulitali mwake chinali mikono 20 mofanana ndi mulifupi mwa nyumbayo ndipo mulifupi mwake chinali mikono 20. Anachikuta ndi golide wabwino wokwana matalente* 600.+
8 Kenako iye anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ Mulitali mwake chinali mikono 20 mofanana ndi mulifupi mwa nyumbayo ndipo mulifupi mwake chinali mikono 20. Anachikuta ndi golide wabwino wokwana matalente* 600.+