1 Mafumu 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inkawatumiza ku Lebanoni m’magulu a anthu 10,000 pamwezi. Kwa mwezi umodzi anthuwo ankakhala ku Lebanoni, ndipo kwa miyezi iwiri ankakhala kwawo.+ Adoniramu+ ndiye anali woyang’anira anthu olembedwa ntchito yokakamizawo.+
14 Inkawatumiza ku Lebanoni m’magulu a anthu 10,000 pamwezi. Kwa mwezi umodzi anthuwo ankakhala ku Lebanoni, ndipo kwa miyezi iwiri ankakhala kwawo.+ Adoniramu+ ndiye anali woyang’anira anthu olembedwa ntchito yokakamizawo.+