Oweruza 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo iye anati: “Tsopano ngati mwandikomera mtima,+ mundisonyeze chizindikiro kuti nditsimikize kuti ndinudi amene mukulankhula nane.+ Yesaya 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Pempha chizindikiro kwa Yehova Mulungu wako.+ Chikhoza kukhala chozama ngati Manda kapena chachitali ngati malo okwera.” Yesaya 38:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa nthawiyi, Hezekiya anati: “Kodi chizindikiro chakuti ndidzapita kunyumba ya Yehova n’chiyani?”+
17 Pamenepo iye anati: “Tsopano ngati mwandikomera mtima,+ mundisonyeze chizindikiro kuti nditsimikize kuti ndinudi amene mukulankhula nane.+
11 “Pempha chizindikiro kwa Yehova Mulungu wako.+ Chikhoza kukhala chozama ngati Manda kapena chachitali ngati malo okwera.”
22 Pa nthawiyi, Hezekiya anati: “Kodi chizindikiro chakuti ndidzapita kunyumba ya Yehova n’chiyani?”+