Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 6:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Tsopano Gidiyoni anauza Mulungu woona kuti: “Kuti ndidziwe kuti mudzapulumutsa Isiraeli kudzera mwa ine, monga mmene mwalonjezera,+

  • Yesaya 37:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 “‘Ichi chidzakhala chizindikiro chanu: Chaka chino mudya mbewu zomera zokha zimene zinagwera pansi.+ Chaka chamawa mudzadya mbewu zongomera zokha, koma chaka chamkuja, anthu inu mudzabzale mbewu n’kukolola, ndipo mudzalime minda ya mpesa n’kudya zipatso zake.+

  • Yesaya 38:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chizindikiro chochokera kwa Yehova, chakuti Yehova adzakwaniritsadi mawu amene walankhula, ndi ichi:+

  • Mateyu 12:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Tsopano alembi ndi Afarisi ena anamupempha kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutionetse chizindikiro.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena