Yesaya 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Kukubwera masiku amene zinthu zonse zimene zili m’nyumba mwako, ndi zonse zimene makolo ako akhala akusunga kufikira lero, anthu adzazitenga n’kupita nazo ku Babulo.+ Palibe chidzatsale,’+ watero Yehova.
6 ‘Kukubwera masiku amene zinthu zonse zimene zili m’nyumba mwako, ndi zonse zimene makolo ako akhala akusunga kufikira lero, anthu adzazitenga n’kupita nazo ku Babulo.+ Palibe chidzatsale,’+ watero Yehova.