Yesaya 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Tamvera, masiku akubwera pamene zinthu zonse zimene zili mʼnyumba mwako ndiponso zonse zimene makolo ako akhala akusunga mpaka lero, anthu adzazitenga nʼkupita nazo ku Babulo. Palibe chidzatsale,’+ watero Yehova.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:6 Yesaya 1, ptsa. 396-397 Mawu a Mulungu, ptsa. 118-120 Nsanja ya Olonda,3/1/1988, ptsa. 29-30
6 ‘Tamvera, masiku akubwera pamene zinthu zonse zimene zili mʼnyumba mwako ndiponso zonse zimene makolo ako akhala akusunga mpaka lero, anthu adzazitenga nʼkupita nazo ku Babulo. Palibe chidzatsale,’+ watero Yehova.+