Yesaya 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Kukubwera masiku amene zinthu zonse zimene zili m’nyumba mwako, ndi zonse zimene makolo ako akhala akusunga kufikira lero, anthu adzazitenga n’kupita nazo ku Babulo.+ Palibe chidzatsale,’+ watero Yehova. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:6 Yesaya 1, ptsa. 396-397 Mawu a Mulungu, ptsa. 118-120 Nsanja ya Olonda,3/1/1988, ptsa. 29-30
6 ‘Kukubwera masiku amene zinthu zonse zimene zili m’nyumba mwako, ndi zonse zimene makolo ako akhala akusunga kufikira lero, anthu adzazitenga n’kupita nazo ku Babulo.+ Palibe chidzatsale,’+ watero Yehova.