-
2 Mafumu 10:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Tsopano iye anauza munthu amene anali kuyang’anira chipinda chosungira zovala kuti: “Tulutsa zovala zoti olambira onse a Baala avale.” Choncho iye anawatulutsiradi zovalazo.
-
-
Nehemiya 7:72Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
72 Zimene anthu ena onse anapereka zinakwana ndalama za dalakima zagolide 20,000, ndalama za mina zasiliva 2,000 ndi mikanjo ya ansembe 67.
-