22 Chotero Hilikiya pamodzi ndi anthu amene mfumu inatchula anapita kukanena zimenezi kwa Hulida+ mneneri wamkazi.+ Hulida anali mkazi wa Salumu yemwe anali wosamalira zovala,+ mwana wa Tikiva, mwana wa Harihasi, ndipo Hulidayo anali kukhala kumbali yatsopano ya mzinda wa Yerusalemu.