2 Mafumu 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Hilikiya+ mkulu wa ansembe anauza Safani+ mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la chilamulo+ m’nyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani, ndipo iye anayamba kuliwerenga.
8 Kenako Hilikiya+ mkulu wa ansembe anauza Safani+ mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la chilamulo+ m’nyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani, ndipo iye anayamba kuliwerenga.