2 Mafumu 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumuyo itangomva mawu a m’buku la chilamulolo, nthawi yomweyo inang’amba zovala zake.+