Yesaya 57:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Wolungama wawonongedwa,+ koma palibe amene zikum’khudza.+ Anthu amene amasonyeza kukoma mtima kosatha akusonkhanitsidwira kwa akufa+ popanda wozindikira kuti munthu wolungamayo wafa ndipo wathawa tsoka.+
57 Wolungama wawonongedwa,+ koma palibe amene zikum’khudza.+ Anthu amene amasonyeza kukoma mtima kosatha akusonkhanitsidwira kwa akufa+ popanda wozindikira kuti munthu wolungamayo wafa ndipo wathawa tsoka.+