1 Mafumu 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+ 2 Mbiri 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso, m’mizinda ya Manase,+ Efuraimu,+ Simiyoni, mpaka Nafitali, ndi m’malo onse owonongedwa ozungulira mizindayi,
28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+
6 Komanso, m’mizinda ya Manase,+ Efuraimu,+ Simiyoni, mpaka Nafitali, ndi m’malo onse owonongedwa ozungulira mizindayi,