Yesaya 57:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye amalowa mumtendere.+ Aliyense woyenda mowongoka+ amapita kukapuma+ m’manda.*+