-
1 Mafumu 13:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Ndiyeno mneneriyo ananyamula mtembo wa munthu wa Mulungu woona uja. Anaukweza pabulu n’kubwerera nawo mpaka kukafika mumzinda wa mneneri wokalambayo, kuti akamulire ndi kumuika m’manda munthuyo.
-