2 Mafumu 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anadalira Yehova Mulungu wa Isiraeli.+ Panalibenso mfumu ina yofanana naye pamafumu onse a Yuda+ amene anakhalapo iye asanakhale mfumu, ngakhalenso amene anakhalapo iye atafa.+
5 Iye anadalira Yehova Mulungu wa Isiraeli.+ Panalibenso mfumu ina yofanana naye pamafumu onse a Yuda+ amene anakhalapo iye asanakhale mfumu, ngakhalenso amene anakhalapo iye atafa.+