2 Mafumu 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Menahemu anatenga ndalama zasilivazo kwa Aisiraeli. Iye anatenga masekeli* 50 a siliva kwa mwamuna aliyense wachuma,+ ndipo anawapereka kwa mfumu ya Asuri. Pamenepo mfumu ya Asuri inabwerera ndipo sinakhale m’dzikomo.
20 Menahemu anatenga ndalama zasilivazo kwa Aisiraeli. Iye anatenga masekeli* 50 a siliva kwa mwamuna aliyense wachuma,+ ndipo anawapereka kwa mfumu ya Asuri. Pamenepo mfumu ya Asuri inabwerera ndipo sinakhale m’dzikomo.