Danieli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’chaka chachitatu cha ufumu wa Yehoyakimu+ mfumu ya Yuda, Nebukadinezara mfumu ya Babulo anabwera ku Yerusalemu ndipo anazungulira mzindawo.+
1 M’chaka chachitatu cha ufumu wa Yehoyakimu+ mfumu ya Yuda, Nebukadinezara mfumu ya Babulo anabwera ku Yerusalemu ndipo anazungulira mzindawo.+