Yeremiya 52:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ena mwa anthu onyozeka a m’dzikolo, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anawasiya kuti akhale olima minda ya mpesa ndi alimi ogwira ntchito mokakamizidwa.+
16 Ena mwa anthu onyozeka a m’dzikolo, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anawasiya kuti akhale olima minda ya mpesa ndi alimi ogwira ntchito mokakamizidwa.+