1 Mafumu 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anapanga zotengera 10+ zamkuwa zokhala ndi mawilo. Chotengera chilichonse chinali mikono inayi m’litali, mikono inayi m’lifupi, ndi mikono itatu kutalika kwake kuchokera pansi kukafika pamwamba. 2 Mbiri 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anapanganso zotengera 10,+ mabeseni 10+ oika pa zotengera,
27 Kenako anapanga zotengera 10+ zamkuwa zokhala ndi mawilo. Chotengera chilichonse chinali mikono inayi m’litali, mikono inayi m’lifupi, ndi mikono itatu kutalika kwake kuchokera pansi kukafika pamwamba.