Ekisodo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Mulungu anati: “Lowetsanso dzanja lako m’malayamo.” Choncho analowetsanso dzanja lake m’malaya. Atalitulutsa anaona kuti lakhalanso bwino ngati poyamba.+
7 Ndiyeno Mulungu anati: “Lowetsanso dzanja lako m’malayamo.” Choncho analowetsanso dzanja lake m’malaya. Atalitulutsa anaona kuti lakhalanso bwino ngati poyamba.+