2 Samueli 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano atumiki a Davide ndi Yowabu, anali kuchokera kunkhondo, atafunkha+ zinthu zambiri. Koma Abineri sanali ndi Davide ku Heburoni popeza anali atanyamuka mwamtendere ndipo anali pa ulendo wake.
22 Tsopano atumiki a Davide ndi Yowabu, anali kuchokera kunkhondo, atafunkha+ zinthu zambiri. Koma Abineri sanali ndi Davide ku Heburoni popeza anali atanyamuka mwamtendere ndipo anali pa ulendo wake.