2 Mafumu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Eliya anayankha mtsogoleri wa asilikali 50 uja kuti: “Ngati ndili munthu wa Mulungu, moto+ utsike kumwamba n’kunyeketsa iweyo ndi asilikali ako 50.” Ndipo moto unatsikadi kumwamba n’kunyeketsa mtsogoleriyo ndi asilikali ake 50.+
10 Koma Eliya anayankha mtsogoleri wa asilikali 50 uja kuti: “Ngati ndili munthu wa Mulungu, moto+ utsike kumwamba n’kunyeketsa iweyo ndi asilikali ako 50.” Ndipo moto unatsikadi kumwamba n’kunyeketsa mtsogoleriyo ndi asilikali ake 50.+