2 Mafumu 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mtumiki+ wa munthu wa Mulungu woona atadzuka m’mawa n’kutuluka panja, anangoona kuti gulu lankhondo lazungulira mzindawo ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo. Nthawi yomweyo mtumikiyo anadandaulira mbuye wake kuti: “Kalanga ine mbuyanga!+ Titani?”
15 Mtumiki+ wa munthu wa Mulungu woona atadzuka m’mawa n’kutuluka panja, anangoona kuti gulu lankhondo lazungulira mzindawo ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo. Nthawi yomweyo mtumikiyo anadandaulira mbuye wake kuti: “Kalanga ine mbuyanga!+ Titani?”