16 Atafika, Eliya anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti: ‘Chifukwa chakuti watumiza anthu+ kukafunsa kwa Baala-zebubu mulungu wa ku Ekironi+ ngati kuti ku Isiraeli kulibe Mulungu amene ungafunsireko mawu ake, sutsika pabedi wakwerapo, chifukwa umwalira ndithu.’”