2 Mafumu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno mngelo+ wa Yehova anauza Eliya wa ku Tisibe+ kuti: “Nyamuka ukakumane ndi amithenga a mfumu ya ku Samariya, ndipo ukawafunse kuti, ‘Kodi ku Isiraeli kulibe Mulungu+ kuti mupite kukafunsa kwa Baala-zebubu mulungu wa ku Ekironi?
3 Ndiyeno mngelo+ wa Yehova anauza Eliya wa ku Tisibe+ kuti: “Nyamuka ukakumane ndi amithenga a mfumu ya ku Samariya, ndipo ukawafunse kuti, ‘Kodi ku Isiraeli kulibe Mulungu+ kuti mupite kukafunsa kwa Baala-zebubu mulungu wa ku Ekironi?