2 Mafumu 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo mngelo wa Yehova anauza Eliya kuti: “Tsika upite naye limodzi, usamuope.”+ Choncho Eliya ananyamuka n’kupita pamodzi ndi mtsogoleri uja kwa mfumu. Machitidwe 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma mngelo wa Yehova+ analankhula kwa Filipo kuti: “Nyamuka ndi kulowera kum’mwera, kumsewu wochokera ku Yerusalemu kupita ku Gaza.” (Umenewu ndi msewu wa m’chipululu.)
15 Pamenepo mngelo wa Yehova anauza Eliya kuti: “Tsika upite naye limodzi, usamuope.”+ Choncho Eliya ananyamuka n’kupita pamodzi ndi mtsogoleri uja kwa mfumu.
26 Koma mngelo wa Yehova+ analankhula kwa Filipo kuti: “Nyamuka ndi kulowera kum’mwera, kumsewu wochokera ku Yerusalemu kupita ku Gaza.” (Umenewu ndi msewu wa m’chipululu.)