Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+

      Ndingaopenso ndani?+

      Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+

      Ndingachitenso mantha ndi ndani?+

  • Yeremiya 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Koma iwe umange m’chiuno+ ndipo upite kukawauza zonse zimene ndikulamule kuti ukawauze. Usagwidwe ndi mantha chifukwa cha iwo,+ kuopera kuti ndingakuchititse kugwidwa ndi mantha pamaso pawo.

  • Ezekieli 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Iwe mwana wa munthu, usawaope.+ Usaope mawu awo ngakhale kuti iwo ndi anthu osamva+ ndipo ali ngati zinthu zokulasa.+ Usaope, ngakhale kuti ukukhala pakati pa zinkhanira.+ Usaope mawu awo+ ndipo usachite mantha ndi nkhope zawo,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena