2 Mafumu 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo mngelo wa Yehova anauza Eliya kuti: “Tsika upite naye limodzi, usamuope.”+ Choncho Eliya ananyamuka n’kupita pamodzi ndi mtsogoleri uja kwa mfumu. Miyambo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuopa anthu n’kumene kumatchera msampha,+ koma wokhulupirira Yehova adzatetezedwa.+ Yeremiya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Koma iwe umange m’chiuno+ ndipo upite kukawauza zonse zimene ndikulamule kuti ukawauze. Usagwidwe ndi mantha chifukwa cha iwo,+ kuopera kuti ndingakuchititse kugwidwa ndi mantha pamaso pawo. Luka 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso ndikukuuzani ndithu, mabwenzi anga,+ Musamaope amene amapha thupi lokha, amene sangathe kuchita zoposa pamenepa.+
15 Pamenepo mngelo wa Yehova anauza Eliya kuti: “Tsika upite naye limodzi, usamuope.”+ Choncho Eliya ananyamuka n’kupita pamodzi ndi mtsogoleri uja kwa mfumu.
17 “Koma iwe umange m’chiuno+ ndipo upite kukawauza zonse zimene ndikulamule kuti ukawauze. Usagwidwe ndi mantha chifukwa cha iwo,+ kuopera kuti ndingakuchititse kugwidwa ndi mantha pamaso pawo.
4 Komanso ndikukuuzani ndithu, mabwenzi anga,+ Musamaope amene amapha thupi lokha, amene sangathe kuchita zoposa pamenepa.+