1 Mafumu 18:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Dzanja la Yehova linali ndi Eliya,+ moti iye anakokera chovala chake m’chiuno n’kuchimanga,+ ndipo anayamba kuthamanga n’kupitirira Ahabu mpaka kukafika ku Yezereeli.+ 2 Mafumu 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nthawi yomweyo Elisa anauza Gehazi+ kuti: “Kokera chovala chako m’chiuno ndipo uchimange.+ Tenga ndodo yangayi+ uzipita. Ukakumana ndi munthu aliyense panjira usamupatse moni,+ ndipo munthu akakupatsa moni, usamuyankhe. Ukaike ndodo yangayi pankhope ya mwanayo.”+ 2 Mafumu 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mneneri Elisa anaitana mmodzi wa ana+ a aneneri n’kumuuza kuti: “Konzeka,*+ nyamula botolo ladothi+ la mafutali m’manja mwako, upite ku Ramoti-giliyadi.+ Yobu 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Takokera chovala chako n’kuchimanga m’chiuno ngati mwamuna wamphamvu.Ndikufuna ndikufunse mafunso ndipo iweyo undiyankhe.+ Luka 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Odala ndi akapolo amene mbuye wawo pofika adzawapeza akudikira!+ Ndithu ndikukuuzani, Iye adzamanga m’chiuno+ mwake ndi kuwakhazika patebulo kuti adye chakudya ndipo adzawatumikira.+ 1 Petulo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Konzekeretsani maganizo anu kuti mugwire ntchito mwamphamvu,+ khalanibe oganiza bwino,+ ndipo ikani chiyembekezo chanu pa kukoma mtima kwakukulu+ kumene kudzafika kwa inu, Yesu Khristu akadzaonekera.*+
46 Dzanja la Yehova linali ndi Eliya,+ moti iye anakokera chovala chake m’chiuno n’kuchimanga,+ ndipo anayamba kuthamanga n’kupitirira Ahabu mpaka kukafika ku Yezereeli.+
29 Nthawi yomweyo Elisa anauza Gehazi+ kuti: “Kokera chovala chako m’chiuno ndipo uchimange.+ Tenga ndodo yangayi+ uzipita. Ukakumana ndi munthu aliyense panjira usamupatse moni,+ ndipo munthu akakupatsa moni, usamuyankhe. Ukaike ndodo yangayi pankhope ya mwanayo.”+
9 Mneneri Elisa anaitana mmodzi wa ana+ a aneneri n’kumuuza kuti: “Konzeka,*+ nyamula botolo ladothi+ la mafutali m’manja mwako, upite ku Ramoti-giliyadi.+
3 Takokera chovala chako n’kuchimanga m’chiuno ngati mwamuna wamphamvu.Ndikufuna ndikufunse mafunso ndipo iweyo undiyankhe.+
37 Odala ndi akapolo amene mbuye wawo pofika adzawapeza akudikira!+ Ndithu ndikukuuzani, Iye adzamanga m’chiuno+ mwake ndi kuwakhazika patebulo kuti adye chakudya ndipo adzawatumikira.+
13 Konzekeretsani maganizo anu kuti mugwire ntchito mwamphamvu,+ khalanibe oganiza bwino,+ ndipo ikani chiyembekezo chanu pa kukoma mtima kwakukulu+ kumene kudzafika kwa inu, Yesu Khristu akadzaonekera.*+