Yobu 40:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Takokera chovala chako n’kuchimanga m’chiuno ngati mwamuna wamphamvu.+Ndikufuna ndikufunse mafunso ndipo iweyo undiyankhe.+
7 “Takokera chovala chako n’kuchimanga m’chiuno ngati mwamuna wamphamvu.+Ndikufuna ndikufunse mafunso ndipo iweyo undiyankhe.+