2 Mafumu 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 M’chaka cha 23 cha Yehoasi+ mwana wa Ahaziya+ mfumu ya Yuda, Yehoahazi+ mwana wa Yehu+ anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya, kwa zaka 17. 2 Mafumu 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehoahazi sanatsale ndi anthu alionse kupatulapo amuna 50 okwera pamahatchi, magaleta 10, ndi asilikali 10,000 oyenda pansi,+ chifukwa mfumu ya Siriya inawawononga+ ndi kuwapondaponda ngati fumbi la popunthira mbewu.+
13 M’chaka cha 23 cha Yehoasi+ mwana wa Ahaziya+ mfumu ya Yuda, Yehoahazi+ mwana wa Yehu+ anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya, kwa zaka 17.
7 Yehoahazi sanatsale ndi anthu alionse kupatulapo amuna 50 okwera pamahatchi, magaleta 10, ndi asilikali 10,000 oyenda pansi,+ chifukwa mfumu ya Siriya inawawononga+ ndi kuwapondaponda ngati fumbi la popunthira mbewu.+