2 Mafumu 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anapitiriza kuchita zolungama pamaso pa Yehova,+ koma osati ngati Davide kholo lake.+ Anachita mogwirizana ndi zonse zimene Yehoasi bambo ake anachita.+ 2 Mbiri 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehoasi+ anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova,+ masiku onse a wansembe Yehoyada.+
3 Iye anapitiriza kuchita zolungama pamaso pa Yehova,+ koma osati ngati Davide kholo lake.+ Anachita mogwirizana ndi zonse zimene Yehoasi bambo ake anachita.+