2 Mbiri 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amaziya anapitiriza kuchita zolungama pamaso pa Yehova,+ koma osati ndi mtima wathunthu.+