1 Mafumu 8:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Mutumikire Yehova Mulungu wathu ndi mtima wathunthu+ mwa kuyenda motsatira malangizo ake ndi kusunga malamulo ake, monga mmene mukuchitira lero.” 1 Mafumu 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene iye anali kukalamba,+ akazi ake anali atapotoza+ mtima wake moti iye anali kutsatira milungu ina.+ Sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu+ monga mmene anachitira Davide bambo ake. 2 Mafumu 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anapitiriza kuchita zolungama pamaso pa Yehova,+ koma osati ngati Davide kholo lake.+ Anachita mogwirizana ndi zonse zimene Yehoasi bambo ake anachita.+ Salimo 78:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Mtima wawo sunali wokhulupirika kwa iye.+Ndipo iwo sanakhulupirike ku pangano lake.+
61 Mutumikire Yehova Mulungu wathu ndi mtima wathunthu+ mwa kuyenda motsatira malangizo ake ndi kusunga malamulo ake, monga mmene mukuchitira lero.”
4 Pamene iye anali kukalamba,+ akazi ake anali atapotoza+ mtima wake moti iye anali kutsatira milungu ina.+ Sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu+ monga mmene anachitira Davide bambo ake.
3 Iye anapitiriza kuchita zolungama pamaso pa Yehova,+ koma osati ngati Davide kholo lake.+ Anachita mogwirizana ndi zonse zimene Yehoasi bambo ake anachita.+