2 Mbiri 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako anthu onse+ a ku Yuda anatenga Uziya+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16, n’kumulonga+ ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+ Mateyu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Asa anabereka Yehosafati.+Yehosafati anabereka Yehoramu.+Yehoramu anabereka Uziya.
26 Kenako anthu onse+ a ku Yuda anatenga Uziya+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16, n’kumulonga+ ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+