2 Mafumu 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Salumu mwana wa Yabesi, anakhala mfumu m’chaka cha 39 cha Uziya+ mfumu ya Yuda. Iye analamulira ku Samariya kwa mwezi umodzi wathunthu.+ Mateyu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Asa anabereka Yehosafati.+Yehosafati anabereka Yehoramu.+Yehoramu anabereka Uziya.
13 Salumu mwana wa Yabesi, anakhala mfumu m’chaka cha 39 cha Uziya+ mfumu ya Yuda. Iye analamulira ku Samariya kwa mwezi umodzi wathunthu.+