2 Mafumu 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako anthu onse a ku Yuda anatenga Azariya,*+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16,+ n’kumulonga ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+ 2 Mafumu 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’chaka cha 27 cha Yerobowamu mfumu ya Isiraeli, Azariya*+ mwana wa Amaziya+ mfumu ya Yuda anakhala mfumu. 1 Mbiri 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehoasi anabereka Amaziya,+ Amaziya anabereka Azariya,+ Azariya anabereka Yotamu,+
21 Kenako anthu onse a ku Yuda anatenga Azariya,*+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16,+ n’kumulonga ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+
15 M’chaka cha 27 cha Yerobowamu mfumu ya Isiraeli, Azariya*+ mwana wa Amaziya+ mfumu ya Yuda anakhala mfumu.