2 Mafumu 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako anthu onse a ku Yuda anatenga Azariya,*+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16,+ n’kumulonga ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+ 2 Mbiri 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uziya+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 16, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 52. Amayi ake anali a ku Yerusalemu, ndipo dzina lawo linali Yekoliya.+ Mateyu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Asa anabereka Yehosafati.+Yehosafati anabereka Yehoramu.+Yehoramu anabereka Uziya.
21 Kenako anthu onse a ku Yuda anatenga Azariya,*+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16,+ n’kumulonga ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+
3 Uziya+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 16, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 52. Amayi ake anali a ku Yerusalemu, ndipo dzina lawo linali Yekoliya.+