2 Mafumu 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Azariya anayamba kulamulira ali ndi zaka 16, ndipo analamulira ku Yerusalemu+ zaka 52. Amayi ake anali a ku Yerusalemu, ndipo dzina lawo linali Yekoliya.
2 Azariya anayamba kulamulira ali ndi zaka 16, ndipo analamulira ku Yerusalemu+ zaka 52. Amayi ake anali a ku Yerusalemu, ndipo dzina lawo linali Yekoliya.