2 Mafumu 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nkhani zina zokhudza Azariya ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda. 2 Mbiri 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nkhani zina zokhudza Yotamu,+ nkhondo zake ndi njira zake zonse, zinalembedwa m’Buku+ la Mafumu a Isiraeli ndi Yuda.
6 Nkhani zina zokhudza Azariya ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.
7 Nkhani zina zokhudza Yotamu,+ nkhondo zake ndi njira zake zonse, zinalembedwa m’Buku+ la Mafumu a Isiraeli ndi Yuda.