Deuteronomo 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Samalani kuti musaiwale+ Yehova Mulungu wanu ndi kusasunga malamulo, zigamulo ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero.+ Ekisodo 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo Mulungu anayamba kulankhula mawu awa, kuti:+ Ekisodo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ndipo izi ndizo zigamulo zoti uwaikire:+
11 Samalani kuti musaiwale+ Yehova Mulungu wanu ndi kusasunga malamulo, zigamulo ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero.+